[00:02.91] Ambuye ati mzabwela ngat mbala [00:14.07] Mzapeza a2 ena atangokhala [00:16.79] Ena Ali ku bar [00:18.36] Ena ali Ku vephi [00:19.96] Ena akuthamanga kukaona nyawu kwa Senti [00:22.33] Akut musanabwele kuzabwela chi Beast [00:25.24] Pachipumi pake pazakhala zma 666 [00:28.11] Nde ndumazifunsa ndekha Chen chen nchit [00:31.18] Akumakambaso zambirmbir scientists [00:34.05] Baibulo lanu a2 analipanga twist [00:36.69] Zosawasangalatsa anapanga delete [00:39.83] Mpingo ulionse ukuona ngt ukukhonza [00:42.79] Sakuziwa mmaziwa zoona nd Yehova [00:45.42] Nde ndmaziwa mbuye muzambwela nd2 yaweh [00:48.36] Kuzati jaja tonse ndipo palibe azathawe [00:51.26] Nde chonde mukazabwela musazandiiwale [00:53.96] Ndine mu2 ochimwa kwambiri koma muzandipase mapiko [00:57.02] Mapiko muzandipase Mapiko ×2 [01:07.45] Ndizauluke nanu ulendo wakumwabamba [01:12.94] Mapiko muzandipase [01:18.82] Aah [01:21.44] Away akut nd a Pastor [01:23.00] A2 akumwa mowa Sawasangalasa [01:25.70] Pa Dziko la Pansi pompa ayamba Ku jaja [01:28.32] Ayiwala ntchito yomwe inu mnawapasa [01:31.23] Gospel yawo akut amayimba okhaokha [01:33.93] Tikayimba nd Wa Secular amayamba kuthoka [01:34.30] Akut uyimba bwanji nd mafana olowelera [01:37.18] Koma mesa Mulungu amafuna Nkhosa zosochela [01:42.47] Aku jaja alowa Mmalo mwanu Namalenga [01:45.65] Kuchosa Chisoso Mmaso mwanga mwawo muli nchenga [01:48.71] Akut nd a Khristu akulu Ife nd tiana [01:51.44] Aku jaja a2 ena [01:54.05] Kona Mmachimwa mosiyana [01:57.56] Koma ndmadziwa mzabwela nd2 yawe [01:59.99] Kuzati jaja tonse ndipo palibe azathewe [02:01.28] Nde mukazabwela chonde msandiwale ndne mu2 ochimwa kwambiri koma [02:02.81] Muzandipase [02:07.89]