Ambuye ati mzabwela ngat mbala Mzapeza a2 ena atangokhala Ena Ali ku bar Ena ali Ku vephi Ena akuthamanga kukaona nyawu kwa Senti Akut musanabwele kuzabwela chi Beast Pachipumi pake pazakhala zma 666 Nde ndumazifunsa ndekha Chen chen nchit Akumakambaso zambirmbir scientists Baibulo lanu a2 analipanga twist Zosawasangalatsa anapanga delete Mpingo ulionse ukuona ngt ukukhonza Sakuziwa mmaziwa zoona nd Yehova Nde ndmaziwa mbuye muzambwela nd2 yaweh Kuzati jaja tonse ndipo palibe azathawe Nde chonde mukazabwela musazandiiwale Ndine mu2 ochimwa kwambiri koma muzandipase mapiko Mapiko muzandipase Mapiko ×2 Ndizauluke nanu ulendo wakumwabamba Mapiko muzandipase Aah Away akut nd a Pastor A2 akumwa mowa Sawasangalasa Pa Dziko la Pansi pompa ayamba Ku jaja Ayiwala ntchito yomwe inu mnawapasa Gospel yawo akut amayimba okhaokha Tikayimba nd Wa Secular amayamba kuthoka Akut uyimba bwanji nd mafana olowelera Koma mesa Mulungu amafuna Nkhosa zosochela Aku jaja alowa Mmalo mwanu Namalenga Kuchosa Chisoso Mmaso mwanga mwawo muli nchenga Akut nd a Khristu akulu Ife nd tiana Aku jaja a2 ena Kona Mmachimwa mosiyana Koma ndmadziwa mzabwela nd2 yawe Kuzati jaja tonse ndipo palibe azathewe Nde mukazabwela chonde msandiwale ndne mu2 ochimwa kwambiri koma Muzandipase