Anthem

歌曲 Anthem
歌手 QUEST
歌手 BurBn
专辑 The Beat Tape - Volume 1

歌词

[00:14.77] Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendere
[00:22.24] Gonjetsani adani, njala, nthenda ndi nsanje, eh
[00:30.06] Where you from? Malawi!
[00:31.55] Pakati ku mpoto ku m'mera?
[00:33.64] Where you from? Malawi!
[00:35.51] M'makonda komwe n'nabadwila
[00:37.06] Where you from? Malawi!
[00:39.11] Pakati ku mpoto ku m'mwera?
[00:41.07] Where you from? Malawi!
[00:42.83] M'makonda komwe n'nabadwila
[00:44.88] Ndimakonda komwe n'nabadwila
[00:47.21] Zakunja sindisilira
[00:48.54] Ndine mtumbuka nde ndimanyadira
[00:50.92] Black girls ndimaiifila
[00:52.21] Wanyane kweni mulinkhuni, eh?
[00:54.86] Tikamwe mowa wa nkhuni, eh
[00:56.76] I am from Malawi phala timamwa la Likuni, eh
[01:00.25] Ndanyamula mbendera mwina dziko ndikusintha
[01:03.51] M'mene zinthu zikuyendera
[01:05.97] Osapusitsika ambuye amatikondela
[01:09.62] Tinjoye tivine gule wankulu (gule wankulu, gule wankulu)
[01:13.59] Azimayi kuliza nthungululu (ilililili)
[01:16.24] Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendere
[01:23.12] Gonjetsani adani, njala, nthenda ndi nsanje, eh
[01:30.57] Where you from? Malawi!
[01:32.59] Pakati ku mpoto ku mmwela?
[01:34.40] Where you from? Malawi!
[01:36.51] M'makonda komwe n'nabadwila
[01:37.92] Where you from? Malawi!
[01:40.02] Pakati ku mpoto ku m'mwera?
[01:41.80] Where you from? Malawi! (Yeah)
[01:43.99] M'makonda komwe n'nabadwila
[01:45.86] Chariz!
[01:46.66] Dziko la mkaka ndi uchi
[01:48.04] Kwabata, sungamve mifuti
[01:50.01] Timapephera nkachisi komaso mzikiti
[01:54.07] Timalima chamba timalima tea
[01:55.71] Tiyendereni dindani passport
[01:57.82] Panga zotheka utenge permit
[01:59.34] Mukhala mwalandilidwa ndekuti, ayy
[02:02.44] Timamwa Malawi Gin
[02:04.11] Ice kuika mchitini
[02:05.75] Lake Malawi too clean
[02:07.48] Nsomba nasiya kudya za nchitini
[02:09.83] Timadya Chambo, Micheni
[02:11.36] Alenje anyamula mipeni
[02:13.45] Dzanja linalo chishango
[02:15.40] Kumbuyo kuli mikondo
[02:17.22] Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendere
[02:24.46] Gonjetsani adani, njala, nthenda ndi nsanje, eh
[02:31.68] Where you from? Malawi!
[02:33.46] Pakati ku mpoto ku m'mera?
[02:35.56] Where you from? Malawi!
[02:37.11] M'makonda komwe n'nabadwira
[02:39.27] Where you from? Malawi!
[02:41.14] Pakati ku mpoto ku m'mwera?
[02:43.10] Where you from? Malawi!
[02:45.17] M'makonda komwe nabadwira
[02:47.55]